Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zanga​—Kugonana, Makhalidwe ndi Chikondi

Mfundo Zanga​—Kugonana, Makhalidwe ndi Chikondi

Gawo 4

Mfundo Zanga​—Kugonana, Makhalidwe ndi Chikondi

Lembani mfundo zitatu zimene mukufuna kuti muzizitsatira. Pa mfundo iliyonse mulembenso chifukwa chake mukuona kuti ndi nzeru kutsatira mfundoyo. *

1. ․․․․․

2. ․․․․․

3. ․․․․․

[Mawu a M’munsi]

^ ndime 3 Mwachitsanzo, “Ndiziyesetsa kupewa kugonana ndi munthu mpaka ndidzalowe m’banja ndipo ndikukhulupirira kuti kuchita zimenezi ndi nzeru chifukwa . . .” Onetsetsani kuti mwalemba zimene inuyo mwasankha kuchita osati kungotengera wina.