Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zanga—Makhalidwe Amene Angawononge Moyo Wanu

Mfundo Zanga—Makhalidwe Amene Angawononge Moyo Wanu

Gawo 5

Mfundo Zanga​—Makhalidwe Amene Angawononge Moyo Wanu

Lembani zinthu zimene zikhoza kukuchititsani kufuna kuyamba kusuta, kumwa mowa kwambiri kapena kugwiritsa ntchito mankhwala osokoneza bongo.

․․․․․

Lembani zinthu zina zabwino zimene mungachite kuti muzikhala osangalala popanda kuchita zinthu zomwe zingawononge moyo wanu.

․․․․․