Mfundo Zanga—Zimene Mumachita pa Nthawi Yopuma
Gawo 6
Mfundo Zanga—Zimene Mumachita pa Nthawi Yopuma
Fotokozani nthawi yomaliza imene makolo anu anakukanizani mutapempha kuti mupite kokasangalala kwinakwake. Lembaninso zimene mukuganiza kuti zimachititsa makolo anu kuti azikukanizani nthawi zina.
․․․․․
Lembani mfundo zimene mwaphunzira m’chigawochi zomwe mukufuna kuti muzitsatira n’cholinga choti makolo anu azikulolani kupita kokasangalala nthawi zina.
․․․․․