Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Chikuto Chakumbuyo

Chikuto Chakumbuyo

Chikuto Chakumbuyo

Zigawo za bukuli zili ndi mitu iyi

KUKHALA NDI MAKOLO KOMANSO ACHIBALE

KHALIDWE LANU

ZOCHITIKA KUSUKULU

KUGONANA, MAKHALIDWE NDIPONSO CHIKONDI

MAKHALIDWE AMENE ANGAWONONGE MOYO WANU

ZIMENE MUMACHITA PA NTHAWI YOPUMA

KULAMBIRA MULUNGU

MAWU AKUMAPETO OPITA KWA MAKOLO

Malangizo othandiza achinyamata. Kodi n’chiyani chingakuthandizeni kuti mukhale ndi makhalidwe abwino omwe angadzakuthandizeni mukadzakula? Buku Loyamba la Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, lingakuthandizeni. Malangizo amene ali m’bukuli ndi ogwirizana ndi mfundo za m’Baibulo. Mawu a Mulungu athandiza anthu mamiliyoni ambiri kulimbana ndi mavuto pa moyo wawo. Werengani bukuli kuti muone mmene lingakuthandizireni.

“Kuganiza bwino kudzakuyang’anira, ndipo kuzindikira kudzakuteteza.”​—Miyambo 2:11.