Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Kukonzekera Kupita Kolalikira

Kukonzekera Kupita Kolalikira

Thandizani Kalebe ndi Sofiya kuti akonzekere kupita kolalikira. Pangani dawunilodi tsambali.

 

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Tiyeni Tikalalikire

Kodi Sofiya watenga zonse zofunika popita kolalikira? Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene inunso muyenera kutenga popita kolalikira.

ZOCHITA PA GAWO LA KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Pangani Chikwama cha mu Utumiki

Kodi mumafunika kutenga chiyani popita kolalikira? Tsambali lingakuthandizeni kuti muzitenga chikwama popita mu utumiki.

ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA

Zoti Ana Achite

Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.