Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo

Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo

MITU

Akufa Adzaukitsidwa 48, 86, 91, 93

Ananu, Muzitumikira Yehova 37, 51, 59, 61, 72, 100

Chifuniro cha Mulungu Chidzachitika Padzikoli Ngati Kumwamba 25, 55, 60, 62, 63, 71, 96, 102

Kudzikonda Kumavutitsa Ifeyo Komanso Anthu Ena 3, 4, 12, 27, 28, 39, 49, 88

Kulambira Konyenga Kumachokera kwa Mdyerekezi 19, 20, 22, 38, 46, 49, 52, 58

Mkwiyo Ndi Woopsa 4, 12, 41, 45, 49, 65, 89

Mukalonjeza Muzikwaniritsa Ngati Yehova 8, 9, 11, 23, 24, 31, 34, 35, 36, 66, 93

Mulungu Amadana ndi Anthu Oukira 7, 17, 26, 27, 28, 88

Musamachite Zoipa 14, 27, 49, 53, 58, 88, 89

Musamataye Mtima Mukakumana ndi Mavuto 16, 47, 51, 57, 64, 75, 90, 95, 99, 101

Musataye Zimene Yehova Wakupatsani 12, 13, 24, 35, 36, 56, 75, 95, 100

Muzikhululukira Anzanu Ngati Yehova 13, 15, 31, 43, 92

Muzimvera Kuti Mukhale ndi Moyo 3, 5, 10, 37, 39, 54, 59, 65, 72

Muziyamika Yehova Nthawi Zonse 2, 6, 67, 103

Nsanje Imadanitsa 4, 14, 41

N’zosatheka Kukonda Mulungu Ngati Simukonda Anzanu 4, 13, 15, 41

Oipa Onse Sadzakhalakonso 5, 10, 32, 46, 102

Simungatumikire Mulungu ndi Chuma pa Nthawi Imodzi 10, 17, 44, 59, 75, 76

Tizigwirizana ndi Anthu Amene Amakonda Yehova 16, 33, 42, 80, 87, 100, 103

Tizilalikira Uthenga Wabwino wa Ufumu 73, 76, 94, 95, 96, 97, 98

Tizimvera Yesu Chifukwa Ndi Mfumu ya Ufumu wa Mulungu 74, 78, 79, 83, 84, 85, 91, 92, 99

Ufumu wa Mulungu Udzapangitsa Kuti Aliyense Azikhala Mosangalala 1, 48, 62, 79, 81, 83, 85, 86

Yehova Adzatithandiza Choncho Tizichita Zinthu Molimba Mtima 40, 47, 51, 53, 57, 61, 64, 65, 76, 88, 101

Yehova Akhale Mnzanu 11, 30, 33, 51, 56, 59, 69, 81, 82

Yehova Amakonda Anthu a Mitundu Yonse 30, 33, 48, 54, 77, 94, 97, 98, 99

Yehova Amamvetsera Tikamapemphera Kuchokera Mumtima 35, 38, 50, 64, 82

Yehova Amaona Kuti Anthu Onse Ndi Amtengo Wapatali 8, 9, 11, 21, 23, 68, 70, 74, 87, 90

Yehova Amateteza Anthu Amene Amamukonda 6, 22, 40, 50, 52, 55, 64, 71, 84

Yehova Amateteza Anthu Odzichepetsa 43, 45, 65, 67, 69

Yehova Amatsogolera Anthu Ake 18, 25, 26, 27, 29, 34, 39, 44, 73, 80

Yehova Analenga Dziko Kuti Tizikhalamo 1, 2, 102, 103

Yehova Anatipatsa Baibulo Kuti Litithandize Kupeza Nzeru 56, 66, 72, 75, 81

Yehova Ndi Wamphamvuyonse 1, 7, 18, 19, 20, 21, 22, 26, 55, 60

Yehova Saiwala Zimene Tamuchitira 16, 29, 32, 48, 65, 69, 77, 100

Yehova Sanama 3, 10, 16, 63, 68, 70, 102, 103