Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

NYIMBO 6

Kumwamba Kumalengeza Ulemerero wa Mulungu

Kumwamba Kumalengeza Ulemerero wa Mulungu

(Salimo 19)

  1. 1. Zakumwamba zimatamanda M’lungu.

    Zomwe analenga

    N’zochititsa chidwi.

    Zimalengeza ulemerero.

    Timazindikira kuti

    Alidi ndi mphamvu.

  2. 2. Malamulo a M’lungu ndi abwino.

    Mawu ake onse

    Amatiteteza.

    Amaweruzanso molungama.

    Mawu ake ndi oona,

    Amatithandiza.

  3. 3. Tiziopa Mulungu mpaka kale.

    Malamulo ake

    Ali ngati nyale

    Ndipotu amatitsogolera.

    Dzina lake loyeralo

    Tililemekeze.