NYIMBO 22 Ufumu Umene Ukulamulira Kumwamba Ubwere Sankhani Zoti Mumvetsere Ufumu Umene Ukulamulira Kumwamba Ubwere Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Chivumbulutso 11:15; 12:10) 1. Yehova Mulungu wathu, Ndinu wamuyaya. Mwapatsa Yesu Ufumu, Mwa kufuna kwanu. Ufumu udzalamula Padziko lonse lapansi. (KOLASI) Zafika tsopano Ufumu chipulumutso. Ufumu wayamba. Tipempha kuti: “Ubwere!” 2. Nthawi ya Satana yatha; Dziko latsopano Lili pafupi kwambiri. Mavuto adzatha. Ufumu udzalamula Padziko lonse lapansi. (KOLASI) Zafika tsopano Ufumu chipulumutso. Ufumu wayamba. Tipempha kuti: “Ubwere!” 3. Angelo asangalala, Aimba mokondwa. Satana wachotsedwako, Onse akondwera. Ufumu udzalamula; Padziko lonse lapansi. (KOLASI) Zafika tsopano Ufumu chipulumutso. Ufumu wayamba. Tipempha kuti: “Ubwere!” (Onaninso Dan. 2:34, 35; 2 Akor. 4:18.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Ufumu Umene Ukulamulira Kumwamba Ubwere IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Ufumu Umene Ukulamulira Kumwamba Ubwere (Nyimbo 22) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ufumu Umene Ukulamulira Kumwamba Ubwere (Nyimbo 22) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016822/sign/wpub/1102016822_sign_sqr_xl.jpg sjj 22