Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

NYIMBO 27

Ana a Mulungu Adzaonekela

Ana a Mulungu Adzaonekela

(Aroma 8:19)

  1. 1. Nthawi yafika Yehova

    Aonetse onse.

    Ana ake osankhiwa

    Na mzimu woyela.

    (KOLASI)

    Ana a Yehova M’lungu

    Adzaonekela.

    Pamodzi na Yesu Mfumu

    Adzalamulila.

  2. 2. Otsalila odzozedwa

    Adzaitanidwa.

    Adzasonkhana pamodzi,

    Na Khristu kumwamba.

    (KOLASI)

    Ana a Yehova M’lungu

    Adzaonekela.

    Pamodzi na Yesu Mfumu

    Adzalamulila.

    (BILIJI)

    Capamodzi adzaononga

    Onse oipa.

    Na cimwemwe, kwa muyaya,

    Adzalamulila.

    (KOLASI)

    Ana a Yehova M’lungu

    Adzaonekela.

    Pamodzi na Yesu Mfumu

    Adzalamulila.

(Onaninso Dan. 2:34, 35;1 Akor. 15:51, 52; 1 Ates. 4:15-17.)