NYIMBO 32 Khalani Okhulupirika kwa Yehova Sankhani Zoti Mumvetsere Khalani Okhulupirika kwa Yehova Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Ekisodo 32:26) 1. Kale tinalitu achisoni, Tinali m’chipembedzo chonyenga; Koma tinasangalala zedi Titamva za Ufumu. (KOLASI) Yenda ndi Yehova; Usangalale. Sangakusiyetu; Yenda m’kuwala. Lengeza uthenga Wamtenderewu. Ufumu wa Khristu Sudzatha konse. 2. Timayenda naye nthawi zonse, Polalikira kwa anthu onse. Pano anthu adzisankhiretu, Kumvera M’lungu wathu. (KOLASI) Yenda ndi Yehova; Usangalale. Sangakusiyetu; Yenda m’kuwala. Lengeza uthenga Wamtenderewu. Ufumu wa Khristu Sudzatha konse. 3. Mdyerekezi Sitidzamuopa. Tidzakhulupirira Yehova. Kaya adani angachuluke, M’lungu ndi mphamvu yathu. (KOLASI) Yenda ndi Yehova; Usangalale. Sangakusiyetu; Yenda m’kuwala. Lengeza uthenga Wamtenderewu. Ufumu wa Khristu Sudzatha konse. (Onaninso Sal. 94:14; Miy. 3:5, 6; Aheb. 13:5.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Khalani Okhulupirika kwa Yehova IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Khalani Okhulupirika kwa Yehova (Nyimbo 32) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Khalani Okhulupirika kwa Yehova (Nyimbo 32) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016832/sign/wpub/1102016832_sign_sqr_xl.jpg sjj 32