Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

NYIMBO 33

Tulila Yehova Nkhawa Zako

Tulila Yehova Nkhawa Zako

(Salimo 55)

  1. 1. Conde nipempha Yehova

    Muniyankhe pemphelo.

    Mvelani kulila kwanga,

    Ndipo nithandizeni.

    (KOLASI)

    Uzani Yehova nkhawa,

    Iye adzakuthandizani.

    Adzakutsogolelani

    Kuti mutetezeke.

  2. 2. Sembe nenze monga nkhunda,

    Sembe nambululuka,

    Kuthaŵa adani anga

    Kuti asanipeze.

    (KOLASI)

    Uzani Yehova nkhawa,

    Iye adzakuthandizani.

    Adzakutsogolelani

    Kuti mutetezeke.

  3. 3. Yehova ‘katitonthoza

    Timapeza mtendele.

    Iye adzatithandiza

    Tisakhale na nkhawa.

    (KOLASI)

    Uzani Yehova nkhawa,

    Iye adzakuthandizani.

    Adzakutsogolelani

    Kuti mutetezeke.

(Onaninso Sal. 22:5; 31:1-24.)