NYIMBO 35 “Muzitsimikizira Kuti Zinthu Zofunika Kwambiri Ndi Ziti” Sankhani Zoti Mumvetsere “Muzitsimikizira Kuti Zinthu Zofunika Kwambiri Ndi Ziti” Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Afilipi 1:10) 1. Kuzindikira kudzatithandiza, Kudziwa zoona, Kudziwa zomwe ndi zofunika, Kuti tizizichita. (KOLASI) Uzidana ndi choipa. Sangalatsa; Mtima wa Mulungu, Madalitso tidzapeza, Tikamachita zofunika. 2. Palibe chofunika kuposa Kulengeza uthenga, Kufufuza a njala ya choonadi N’kuwaphunzitsa. (KOLASI) Uzidana ndi choipa. Sangalatsa; Mtima wa Mulungu, Madalitso tidzapeza, Tikamachita zofunika. 3. Tikamachita zofunika, Tidzakhala okhutira. Mtendere wa Mulungu Udzatetezatu maganizo. (KOLASI) Uzidana ndi choipa. Sangalatsa; Mtima wa Mulungu, Madalitso tidzapeza, Tikamachita zofunika. (Onaninso Sal. 97:10; Yoh. 21:15-17; Afil. 4:7.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena “Muzitsimikizira Kuti Zinthu Zofunika Kwambiri Ndi Ziti” IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA “Muzitsimikizira Kuti Zinthu Zofunika Kwambiri Ndi Ziti” (Nyimbo 35) Chinenero Chamanja cha ku Malawi “Muzitsimikizira Kuti Zinthu Zofunika Kwambiri Ndi Ziti” (Nyimbo 35) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016835/sign/wpub/1102016835_sign_sqr_xl.jpg sjj 35