NYIMBO 40 Kodi Ndife a Ndani? Sankhani Zoti Mumvetsere Kodi Ndife a Ndani? Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Aroma 14:8) 1. Iwe ndi wandani? Umvera m’lungu uti? Amene umam’gwadirayo. Iye ndiye m’lungu wako. Milungu iwiri; Sungaitumikire. Sungalambire iwiri yonse, Sankhapo mmodzi yekha. 2. Iwe ndi wandani? Umvera m’lungu uti? Zilitu ndi iwe kusankha, Woona kaya wonama. Kodi Kaisara Udakamukondabe? Kapena udzamvera Yehova N’kugwira ntchito yake? 3. Ine ndi wandani? Ndidzamvera Yehova. Atate wanga wakumwamba; Ine ndidzam’sangalatsa. Anandigulatu; Ndidzamutumikira. Ndizim’lambira, dzina lakenso Ndizililemekeza. (Onaninso Yos. 24:15; Sal. 116:14, 18; 2 Tim. 2:19.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kodi Ndife a Ndani? IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Kodi Ndife a Ndani? (Nyimbo 40) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kodi Ndife a Ndani? (Nyimbo 40) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016840/sign/wpub/1102016840_sign_sqr_xl.jpg sjj 40