Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

NYIMBO 51

Tadzipeleka kwa Mulungu

Tadzipeleka kwa Mulungu

(Mateyu 16:24)

  1. 1. M’lungu wathu watikokera kwa Khristu

    Kuti azititsogolera.

    Tadziwa choonadi

    M’lungu watiphunzitsa.

    Tikufuna kuchita

    Zofuna zake zokha.

    (KOLASI)

    Tadzipereka kwa Yehova Mulungu.

    Ndife osangalala kwambiri

  2. 2. Tamulonjeza Yehova mu pemphero

    Kuti tizimutumikira.

    Tilidi ndi chimwemwe.

    Timauzanso ena

    Za dzina la Yehova

    Ndi Ufumu wakenso.

    (KOLASI)

    Tadzipereka kwa Yehova Mulungu.

    Ndife osangalala kwambiri