Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

NYIMBO 79

Aphunzitseni Kucilimika

Aphunzitseni Kucilimika

(Mateyu 28:19, 20)

  1. 1. Tikondwa kuphunzitsa anthu

    Okonda coonadi.

    Onani mmene akulila

    M’njila ya coonadi.

    (KOLASI)

    Yehova, mvelani pempho

    Lakuti muŵasamale

    Mu dzina la Yesu Khristu

    Tipemphela akhale ocilimika.

  2. 2. Tinali kuŵapemphelela

    M’mavuto awo onse.

    Tinali kuŵasamalila.

    Yehova ‘wadalitsa.

    (KOLASI)

    Yehova, mvelani pempho

    Lakuti muŵasamale

    Mu dzina la Yesu Khristu

    Tipemphela akhale ocilimika.

  3. 3. Akhale odalila M’lungu,

    Na Mwana wake Yesu.

    Amvele ndipo apilile,

    Tifuna apambane.

    (KOLASI)

    Yehova, mvelani pempho

    Lakuti muŵasamale

    Mu dzina la Yesu Khristu

    Tipemphela akhale ocilimika.

(Onaninso Luka 6:48; Mac. 5:42; Afil. 4:1.)