Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

NYIMBO 89

Mvera Kuti Udalitsidwe

Mvera Kuti Udalitsidwe

(Luka 11:28)

  1. 1. Kodi timamveradi Yesu Khritsu

    Pa zonse zimene ananena?

    Zomwe anaphunzitsa ndi zabwino.

    Tikamumvera tidalitsidwa.

    (KOLASI)

    Mvera udalitsidwe

    Kuti usangalale.

    Zomwe Mulungu angakuuze,

    Mvera udalitsidwe.

  2. 2. Monga nyumba yomangidwa pathanthwe

    Osati yomangidwa pamchenga,

    Zochita zathu zingatiteteze

    Ngati timamvera Yesu Khristu.

    (KOLASI)

    Mvera udalitsidwe

    Kuti usangalale.

    Zomwe Mulungu angakuuze,

    Mvera udalitsidwe.

  3. 3. Monga mtengo wamumbali mwa madzi

    Umabereka mu nyengo yake,

    Tikamamvera tidzadalitsidwa.

    Tidzalandira moyo wosatha.

    (KOLASI)

    Mvera udalitsidwe

    Kuti usangalale.

    Zomwe Mulungu angakuuze,

    Mvera udalitsidwe.