NYIMBO 89 Khalani Omvera Kuti Mulandire Madalitso Sankhani Zoti Mumvetsere Khalani Omvera Kuti Mulandire Madalitso Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Luka 11:28) 1. Kodi timamveradi Yesu Khristu Pa zonse zimene ananena? Zomwe anaphunzitsa ndi zabwino. Tidalitsidwa tikazimvera. (KOLASI) Mvera udalitsidwe Kuti usangalale. Zomwe Mulungu angakuuze, Mvera udalitsidwe. 2. Monga nyumba yomangidwa pathanthwe Osati yomangidwa pamchenga. Zochita zathu zingatiteteze, Kokha ngati Yesu timumvera. (KOLASI) Mvera udalitsidwe Kuti usangalale. Zomwe Mulungu angakuuze, Mvera udalitsidwe. 3. Monga mtengo wamumbali mwa madzi Umabereka nthawi ’kafika, Tikamvera tidzadalitsidwadi, Moyo wosatha tidzalandira. (KOLASI) Mvera udalitsidwe Kuti usangalale. Zomwe Mulungu angakuuze, Mvera udalitsidwe. (Onaninso Deut. 28:2; Sal. 1:3; Miy. 10:22; Mat. 7:24-27; Luka 6:47-49.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Khalani Omvera Kuti Mulandire Madalitso IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Khalani Omvera Kuti Mulandire Madalitso (Nyimbo 89) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Khalani Omvera Kuti Mulandire Madalitso (Nyimbo 89) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016889/sign/wpub/1102016889_sign_sqr_xl.jpg sjj 89