NYIMBO 94 Timayamikira Mulungu Potipatsa Mawu Ake Sankhani Zoti Mumvetsere Timayamikira Mulungu Potipatsa Mawu Ake Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Afilipi 2:16) 1. Yehova Atate, tikuthokoza Chifukwa Mawu anu mwatipatsa. Munawauziradi; Anatimasula. Kuwala kwake kwatipatsa nzeru. 2. Mawu anu ndi amphamvu kwambiri. Maganizo n’zolinga ’lekanitsa. Ndiponso malamulo, Anu n’ngolungama. Mfundo zanu zimatitsogolera. 3. Mawu anu M’lungu, amatikhudza. Aneneri anu anali anthu, Chonde tithandizeni Tikhulupirire. Mwatipatsa Mawu, tathokoza Ya. (Onaninso Sal. 19:9; 119:16, 162; 2 Tim. 3:16; Yak. 5:17; 2 Pet. 1:21.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Timayamikira Mulungu Potipatsa Mawu Ake IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Timayamikira Mulungu Potipatsa Mawu Ake (Nyimbo 94) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Timayamikira Mulungu Potipatsa Mawu Ake (Nyimbo 94) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016894/sign/wpub/1102016894_sign_sqr_xl.jpg sjj 94