NYIMBO 95 Kuwala Kukuwonjezerekabe Sankhani Zoti Mumvetsere Kuwala Kukuwonjezerekabe Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Miyambo 4:18) 1. Aneneri akale ankafuna, Kudziwa za Yesu Mesiya. Mzimu wa M’lungu unaneneratu, Kuti adzatipulumutsa. Nthawi yakwana, akulamulira, Umboni wake ulipo. Kudziwa zimenezi ndi mwayi Waukulu womwe tili nawo. (KOLASI) Kuwala kwa panjira yathu; Kukuwonjezerekadi. Zomwe M’lungu akuulula; Zimatitsogoleradi. 2. Ambuye wathu wasankha kapolo, Ndi mmene amatidyetsera. Ndipo kuwala kwa cho’nadi pano Kukungowonjezerekabe. Pano tikuyenda molimba mtima, Mowala ngati masana. Tikuthokoza Yehova chifukwa, Cho’nadi chake watipatsa. (KOLASI) Kuwala kwa panjira yathu; Kukuwonjezerekadi. Zomwe M’lungu akuulula; Zimatitsogoleradi. (Onaninso Aroma 8:22; 1 Akor. 2:10; 1 Pet. 1:12.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kuwala Kukuwonjezerekabe IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Kuwala Kukuwonjezerekabe (Nyimbo 95) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kuwala Kukuwonjezerekabe (Nyimbo 95) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016895/sign/wpub/1102016895_sign_sqr_xl.jpg sjj 95