Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

NYIMBO 120

Tikhale Ofatsa Ngati Khristu

Tikhale Ofatsa Ngati Khristu

(Mateyu 11:​28-30)

  1. 1. Yesu anali munthu wapadera

    Koma sanadzikuze, sananyade.

    Anali ndi udindo wapamwamba

    Komatu anali wodzichepetsa.

  2. 2. Kwa anthu omwe ali ndi mavuto,

    Yesu walonjeza kuwathandiza.

    Akamaika Ufumu poyamba

    Iye aziwachitira chifundo.

  3. 3. Yesu anati: ‘Tonse ndi abale.’

    Timamumvera monga Mutu wathu.

    Ofatsa ndi ofunika kwa M’lungu,

    Adzalandira dziko latsopano.