NYIMBO 139 Yerekezerani Kuti Muli M’dziko Latsopano Sankhani Zoti Mumvetsere Yerekezerani Kuti Muli M’dziko Latsopano Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Chivumbulutso 21:1-5) 1. Yerekeza ukuona; Iwe ndi ’ne m’dziko latsopano. Ona mmene udzamvere Kukhala m’dziko lamtendere. Oipa onse achoka. M’lungu wathu sadzalephera. Kusintha zonse padziko lapansi, Tidzamuimbira nyimbo tikumati: (KOLASI) “Tikuthokoza mwachita bwino. Zonse zakhaladi zatsopano. Tikuimba nyimbo mwachisangalalo Ndinudi woyenera ulemerero.” 2. Taganizira m’tsogolo; Iwe ndi ’ne m’dziko latsopano. Sitidzamva ndi kuona Zinthu zotichititsa mantha. Mmene analonjezera; Zinthu zonse zachitikadi. Tsopano aku’kitsanso akufa; Iwo ndi ife tidzamuyamikira: (KOLASI) “Tikuthokoza mwachita bwino. Zonse zakhaladi zatsopano. Tikuimba nyimbo mwachisangalalo Ndinudi woyenera ulemerero.” (Onaninso Sal. 37:10, 11; Yes. 65:17; Yoh. 5:28; 2 Pet. 3:13.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Yerekezerani Kuti Muli M’dziko Latsopano IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Yerekezerani Kuti Muli M’dziko Latsopano (Nyimbo 139) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Yerekezerani Kuti Muli M’dziko Latsopano (Nyimbo 139) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016939/sign/wpub/1102016939_sign_sqr_xl.jpg sjj 139