Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

BOKOSI 8B

Maulosi Atatu Okhudza Mesiya

Maulosi Atatu Okhudza Mesiya

1. “Amene Ali Woyenerera Mwalamulo” (Ezekieli 21:25-27)

NTHAWI ZA ANTHU AKUNJA (607 B.C.E.–1914 C.E.)

  1. 607 B.C.E.​—Zedekiya anachotsedwa pa ufumu

  2. 1914 C.E.​—Yesu amene ndi “woyenerera mwalamulo” kukhala Mfumu komanso Mesiya anaikidwa kukhala Mfumu ndipo anakhala M’busa ndiponso Wolamulira

Bwererani ku mutu 8, ndime 12-15

2. “Mtumiki Wanga . . . Adzawadyetsa Komanso Adzakhala M’busa Wawo” (Ezekieli 34:22-24)

MASIKU OTSIRIZA (1914 C.E.–PAMBUYO PA ARAMAGEDO)

  1. 1914 C.E.​—Yesu amene ndi “woyenerera mwalamulo” kukhala Mfumu komanso Mesiya anaikidwa kukhala Mfumu ndipo anakhala M’busa ndiponso Wolamulira

  2. 1919 C.E.​—Kapolo wokhulupirika komanso wanzeru anasankhidwa kuti aziweta nkhosa za Mulungu

    Akhristu odzozedwa okhulupirika anasonkhanitsidwa pamodzi ndi Mesiya yemwenso ndi Mfumu, ndipo kenako anakhala gulu limodzi ndi a khamu lalikulu

  3. PAMBUYO PA ARAMAGEDO​—Madalitso amene adzakhalepo Mfumu ikamadzalamulira adzakhalapo mpaka kalekale

Bwererani ku mutu 8, ndime 18-22

3. “Onsewo Adzalamuliridwa ndi Mfumu Imodzi” Mpaka Kalekale (Ezekieli 37:22, 24-28)