Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

BOKOSI 9C

Yehova Amakwaniritsa Malonjezo Ake—Masiku Ano

Yehova Amakwaniritsa Malonjezo Ake—Masiku Ano
  • 1. Kulambira koyera kosaphatikizana ndi kulambira mafano

  • 2. Njala yauzimu inatha

  • 3. Ankapereka nsembe zotamanda Mulungu

  • 4. Anasankha amuna okhulupirika kuti azitsogolera

  • 5. Anthu akulambira Mulungu padziko lonse mogwirizana