Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tsiku Loyamba

Tsiku Loyamba

“MULUNGU AMAKUPHUNZITSANI KUKONDANA”​—1 1 ATESALONIKA 4:9

KUM’MAŴA

  • 8:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 8:30 Nyimbo Na. 105 na Pemphelo

  • 8:40 NKHANI YA CHEYAMANI: “Cikondi Sicitha”—Motani? (Aroma 8:38, 39; 1 Akorinto 13:1-3, 8, 13)

  • 9:15 YOSIILANA: Samalani Kuti Musadalile Zinthu Zosakhalitsa

    • Cuma (Mateyu 6:24)

    • Kuchuka (Mlaliki 2:16; Aroma 12:16)

    • Nzelu za Anthu (Aroma 12:1, 2)

    • Mphamvu na Kukongola (Miyambo 31:30; 1 Petulo 3:3, 4)

  • 10:05 Nyimbo Na. 40 na Zilengezo

  • 10:15 KUŴELENGA BAIBO MWAUMOYO: Yehova Anapitilizabe Kuonetsa Kukoma Mtima Kosatha (Genesis 37:1-36; 39:1–47:12)

  • 10:45 Yehova Amakonda Aja Okonda Mwana Wake (Mateyu 25:40; Yohane 14:21; 16:27)

  • 11:15 Nyimbo Na. 20 na Kupumula

KUMASANA

  • 12:25 Vidiyo ya Nyimbo

  • 12:35 Nyimbo Na. 107

  • 12:40 YOSIILANA: Cikondi Sicitha Olo Kuti . . .

    • Tinakulila M’banja Lopanda Cikondi (Salimo 27:10)

    • Anzanu ku Nchito Alibe Cikondi (1 Petulo 2:18-20)

    • Anzanu ku Sukulu Ali na Makhalidwe Oipa (1 Timoteyo 4:12)

    • Mudwala Matenda Osatha (2 Akorinto 12:9, 10)

    • Ndimwe Osauka (Afilipi 4:12, 13)

    • Mutsutsidwa M’banja (Mateyu 5:44)

  • 13:50 Nyimbo Na. 141 na Zilengezo

  • 14:00 YOSIILANA: Cilengedwe Cimaonetsa Cikondi ca Yehova

    • Za Kuthambo (Salimo 8:3, 4; 33:6)

    • Dziko Lapansi (Salimo 37:29; 115:16)

    • Zomela (Genesis 1:11, 29; 2:9, 15; Machitidwe 14:16, 17)

    • Nyama (Genesis 1:27; Mateyu 6:26)

    • Thupi la Munthu (Salimo 139:14; Mlaliki 3:11)

  • 14:55 “Yehova Amalanga Aliyense Amene Iye Amamukonda” (Aheberi 12:5-11; Salimo 19:7, 8, 11)

  • 15:15 “Valani Cikondi” (Akolose 3:12-14)

  • 15:50 Nyimbo Na. 130 na Pemphelo Lothela