Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Ufumu wa Mulungu Unayamba Kulamulila mu 1914

Ufumu wa Mulungu Unayamba Kulamulila mu 1914

Onani mmene ulosi wa m’Baibo umaonetsela kuti 1914 ni caka cimene Ufumu wa Mulungu unayamba kulamulila kumwamba, ndiponso caka cimene “masiku otsiliza” anayamba.—2 Timoteyo 3:1.