Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Dziko Linasintha Kuyambila mu 1914

Dziko Linasintha Kuyambila mu 1914

Baibo inafotokozelatu zocitika komanso makhalidwe a anthu amene adzaonetsa kuti tili ‘m’masiku otsiliza.’ (2 Timoteyo 3:1) Onani mmene zizindikilo za masiku otsiliza zimenezi zaonekela bwino kuyambila mu 1914.