Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Danieli Anali Munthu Wachikhulupiriro Cholimba​—Mbali Yachiwiri

Danieli Anali Munthu Wachikhulupiriro Cholimba​—Mbali Yachiwiri

Ufumu wina wamphamvu wagonjetsa Babulo n’kuyamba kulamulira ndipo Danieli wakumana ndi adani ena atsopano. Chikhulupiriro chake chikuyesedwa kwambiri kuposa poyamba.