Gawo 2 YAMBANI Gawo 2 Ya Mawu Ya Manotsi Cholinga chake: Kukambirana zimene Mulungu watichitira komanso kulambira kumene kumamusangalatsa PHUNZIRO 13 Zipembedzo Zonyenga Zimaphunzitsa Zabodza Zokhudza Mulungu 14 Tingatani Kuti Mulungu Azisangalala Ndi Kulambira Kwathu? 15 Kodi Yesu Ndi Ndani? 16 Kodi Yesu Anachita Zotani Ali Padzikoli? 17 Kodi Yesu Ali Ndi Makhalidwe Otani? 18 Kodi Akhristu Enieni Mungawadziwe Bwanji? 19 Kodi a Mboni za Yehova Ndi Akhristu Enieni? 20 Kodi Mpingo wa Chikhristu Umayendetsedwa Bwanji? 21 Ndi Ndani Amene Amalalikira Uthenga Wabwino? 22 Zimene Mungachite Kuti Muziuzako Ena Uthenga Wabwino 23 Ubatizo Ungakuthandizeni Kukhala Ndi Tsogolo Labwino 24 Kodi Angelo Ndi Ndani Nanga Amachita Chiyani? 25 Kodi Cholinga cha Mulungu Ndi Choti Tikhale Ndi Moyo Wotani? 26 N’chifukwa Chiyani Anthu Amavutika? 27 Kodi Imfa ya Yesu Ingatipulumutse Bwanji? 28 Muziyamikira Zimene Yehova Ndi Yesu Anakuchitirani 29 N’chiyani Chimachitikira Munthu Amene Wamwalira? 30 Achibale Anu Ndi Anzanu Amene Anamwalira Adzakhalanso Ndi Moyo 31 Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani? 32 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira Panopa 33 Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Zotani? Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI Kodi Phunziro la Baibulo lomwe a Mboni za Yehova Amachititsa Limakhala Lotani? Mukamaphunzira Baibulo kwaulere ndi a Mboni za Yehova, mungagwiritse ntchito Baibulo lililonse limene mukufuna. Mungapemphenso onse a m’banja lanu kapena mnzanu wina aliyense kuti akhale nanu pa phunzirolo. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Gawo 2 MUNGAKHALE NDI MOYO MPAKA KALEKALE—KUPHUNZIRA BAIBULO MOKAMBIRANA Gawo 2 Chichewa Gawo 2 https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102021320/univ/art/1102021320_univ_sqr_xl.jpg lff