Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Anthu Ocheza Nawo

Anthu Ocheza Nawo

Kodi anthu ofunika kwambiri omwe munthu angamacheze nawo ndi ati?

Sl 25:14; Yoh 15:13-15; Yak 2:23

Onaninso Miy 3:32

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ge 5:22-24​—Inoki anali pa ubwenzi wolimba ndi Mulungu

    • Ge 6:9​—Nowa anayenda ndi Mulungu mofanana ndi agogo ake a Inoki

N’chifukwa chiyani timafunikira mabwenzi abwino?

Miy 13:20; 17:17; 18:24; 27:17

Onaninso Miy 18:1

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

N’chifukwa chiyani tiyenera kumasonkhana nthawi zonse ndi Akhristu anzathu?

Kodi mungatani kuti mupeze anzanu abwino komanso kuti inuyo mukhale bwenzi labwino kwa ena?

Kodi ndi mavuto ena ati amene tingakumane nawo chifukwa chocheza ndi anthu omwe sakonda Yehova?

Miy 13:20; 1Ak 15:33; Aef 5:6-9

Onaninso 1Pe 4:3-5; 1Yo 2:15-17

Onaninso “Kukonda Dziko

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ge 34:1, 2​—Dina anakumana ndi mavuto chifukwa chosankha kucheza ndi anthu oipa

    • 2Mb 18:1-3; 19:1, 2:​—Yehova anauza Yehosafati yemwe anali mfumu yabwino, kuti asachite mgwirizano ndi Ahabu yemwe anali mfumu yoipa

Kodi tiyenera kupewa kumacheza ndi aliyense amene satumikira Yehova Mulungu?

N’chifukwa chiyani n’kulakwa kukwatirana ndi munthu yemwe sanadzipereke kwa Yehova komanso kubatizidwa?

Onani “Ukwati

N’chifukwa chiyani tiyenera kupewa kumacheza ndi anthu omwe anachotsedwa mumpingo wa Chikhristu?