Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kudzitama

Kudzitama

Sl 94:4; 1Ak 13:4; Yak 3:5, 14

Onaninso Miy 21:24; Yer 9:23, 24

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Owe 7:1-7​—Yehova anachepetsa asilikali a Gidiyoni kuti atsale 300 n’cholinga chofuna kumuthandiza kudziwa kuti Yehova ndi amene adzachititse kuti apambane nkhondoyo.

    • 2Mf 18:28-35​—Senakeribu Mfumu ya Asuri, inagwiritsa ntchito nthumwi yake polankhula modzitama kuti Yehova sangapulumutse Yerusalemu m’manja mwa Asuri