Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kupatsa

Kupatsa

N’chiyani chikusonyeza kuti Yehova amapereka mowolowa manja kuposa wina aliyense?

Kodi ndi zinthu ziti zimene Mulungu sasangalala nazo pa nkhani yopatsa?

Mt 6:1, 2; 2Ak 9:7; 1Pe 4:9

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ge 4:3-7; 1Yo 3:11, 12​—N’chifukwa chiyani Mulungu sanasangalale ndi nsembe ya Kaini?

    • Mac 5:1-11​—Hananiya ndi Safira analangidwa chifukwa chonena bodza lokhudza mphatso yomwe anapereka komanso chifukwa chokhala ndi zolinga zolakwika

Kodi Mulungu amasangalala ndi kupereka kotani?

Mt 6:3, 4; Aro 12:8; 2Ak 9:7; Ahe 13:16

Onaninso Mac 20:35

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Lu 21:1-4​—Yesu anayamikira mayi wamasiye yemwe anali wosauka chifukwa chopereka mosaumira ngakhale kuti anali ndi zochepa

Kodi mpingo wa Chikhristu m’nthawi ya Atumwi unakonza dongosolo lotani lokhudza zopereka?

Mac 11:29, 30; Aro 15:25-27; 1Ak 16:1-3; 2Ak 9:5, 7

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Mac 4:34, 35​—Mpingo wa Chikhristu unkapereka mosaumira ndipo atumwi ankaonetsetsa kuti ndalama zikuperekedwa kwa anthu ovutika

    • 2Ak 8:1, 4, 6, 14​—Mpingo unakonza zoti anthu ovutika azipatsidwa chithandizo

Kodi Akhristu ali ndi udindo wofunika uti pa banja lawo komanso kwa abale ndi alongo mumpingo?

Kodi Baibulo limatiphunzitsa kuti tizichita chiyani kwa anthu osauka?

N’chiyani chikusonyeza kuti anthu amafunikira kwambiri kuthandizidwa mwauzimu kuposa china chilichonse?

Mt 5:3, 6; Yoh 6:26, 27; 1Ak 9:23

Onaninso Miy 2:1-5; 3:13; Mla 7:12; Mt 11:4, 5; 24:14

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Lu 10:39-42​—Yesu anathandiza Marita kuzindikira mfundo yakuti zinthu zauzimu ziyenera kukhala pamalo oyamba