Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Akhristu

Akhristu

Kodi otsatira a Yesu anayamba bwanji kudziwika kuti Akhristu?

Kodi Akhristu oona tingawadziwe bwanji?

Kodi chipulumutso cha Akhristu oona chimachokera kuti?

N’chifukwa chiyani Akhristu amagonjera Khristu monga Mfumu yawo yakumwamba?

N’chifukwa chiyani Akhristu oona amapewa kulowerera m’zochitika za dzikoli?

N’chifukwa chiyani Akhristu oona amamvera maboma a anthu?

Aro 13:1, 6, 7; Tit 3:1; 1Pe 2:13, 14

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Mt 22:15-22​—Yesu anafotokoza chifukwa chake otsatira ake ayenera kumapereka msonkho

    • Mac 4:19, 20; 5:27-29​—Otsatira a Yesu anasonyeza kuti ankamvera maboma a anthu pokhapokha ngati sankawalepheretsa kumvera Mulungu

Kodi Akhristu amafanana ndi asilikali m’njira ziti?

N’chifukwa chiyani Akhristu ayenera kumachita zinthu mogwirizana ndi zimene amakhulupirira?

Mt 5:16; Tit 2:6-8; 1Pe 2:12

Onaninso Aef 4:17, 19-24; Yak 3:13

  • Nkhani ya m’Baibulo yomwe ingakuthandizeni:

    • Mac 9:1, 2; 19:9, 23​—Kulambira kwa Akhristu kumatchedwa “Njira,” kutanthauza kuti zimene Akhristu amachita pa moyo wawo ziyenera kugwirizana ndi zimene Yesu ankachita

N’chifukwa chiyani Akhristu oona ayenera kumachitira umboni za Yehova Mulungu?

N’chifukwa chiyani Akhristu oona amachitiranso umboni za Yesu Khristu?

N’chifukwa chiyani Akhristu oona onse ayenera kumalalikira uthenga wabwino?

Kodi Akhristu ayenera kukhala ndi maganizo otani akamazunzidwa?

Onaninso “Chizunzo

Kodi Akhristu oona onse amaitanidwa kuti akakhale limodzi ndi Yesu Khristu kumwamba?

Kodi Akhristu oona ambiri ali ndi chiyembekezo chotani?

Kodi Akhristu oona amapezekanso m’zipembedzo zonse zimene zimati ndi za Chikhristu?

Kodi anthu onse amene amati ndi Akhristu ndi ophunziradi a Yesu?

Mt 7:21-23; Aro 16:17, 18; 2Ak 11:13-15; 2Pe 2:1

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Mt 13:24-30, 36-43​—Yesu ananena fanizo losonyeza kuti kudzakhala Akhristu abodza ambiri

    • 2Ak 11:24-26​—Mtumwi Paulo ananenanso za “abale achinyengo” pamndandanda wa zinthu zoopsa zimene anakumana nazo

    • 1Yo 2:18, 19​—Mtumwi Yohane anachenjeza za “okana Khristu ambiri” amene pa nthawiyo anali atasiya kale choonadi