Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kukhulupirira Yehova

Kukhulupirira Yehova

Miy 3:5, 21-26; Yes 26:3, 4; Yer 17:7, 8

Onaninso Sl 34:8; 40:4, 5; Miy 20:22; Yes 30:15

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 1Mb 5:18-20, 22​—Mitundu ina ya ana a Isiraeli inagonjetsa adani awo chifukwa chokhulupirira Yehova

    • 2Mb 14:9-13​—Mfumu Asa anapemphera kwa Yehova komanso anasonyeza kuti anali chikhulupiriro cholimba kuti Yehova amuthandiza pa nthawi imene ankaopsezedwa ndi adani