Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kukhutira

Kukhutira

Miy 30:8, 9; 1Ti 6:6-8; Ahe 13:5

Onaninso Mt 6:11, 19-21, 24-33; Mac 20:35; Afi 4:11-13

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 1Mf 17:8-16​—Podalitsa mayi wamasiye wa ku Zarefati, Yehova sanamupatse zinthu zakuthupi zambiri koma ankamupatsa chakudya chokwanira tsiku lililonse. Chozizwitsa chimenechi chingatithandize kwambiri masiku ano pa nkhani yokhutira ndi zimene tili nazo