Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kuchotsa Osalapa

Kuchotsa Osalapa

N’chifukwa chiyani akulu ayenera kuteteza mpingo ku zinthu zoipa?

Kodi khalidwe loipa la m’bale kapena mlongo lingakhudze bwanji mpingo wonse?

1Ak 5:1, 2, 5, 6

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Yos 7:1, 4-14, 20-26​—Tchimo limene Kaini ndi banja lake anachita linachititsa kuti mtundu wonse ukumane ndi mavuto

    • Yon 1:1-16​—Mneneri Yona akanaphetsa anthu onse omwe anali naye muboti chifukwa cha kusamvera kwake

Kodi Mkhristu ayenera kupewa makhalidwe ati kuti asachotsedwe mumpingo?

N’chiyani chiyenera kuchitika ngati Mkhristu wobatizidwa akupitirizabe kuchita tchimo lalikulu?

Kodi ndi zinthu ziti zimene akulu ayenera kufufuza asanagamule mlandu womwe akuweruza?

Kodi akulu omwe ali mukomiti yoweruza mlandu amadziwa bwanji kuti munthu wachita tchimo lalikulu?

N’chifukwa chiyani kuchotsa kapena kudzudzula anthu ena mumpingo n’koyenera? Nanga zimenezi zingathandize bwanji mpingo?

Kodi Baibulo limanena kuti tizichita bwanji zinthu ndi anthu ochotsedwa?

Kodi munthu yemwe anachotsedwa akalapa, zingatheke kuti abwerere mumpingo?

2Ak 2:6, 7

Onaninso “Kulapa

Kodi tonsefe tingathandize bwanji kuti mpingo upitirize kukhala woyera?

N’chifukwa chiyani kungakhale kulakwitsa ngati Mkhristu atabisa tchimo lalikulu mwina chifukwa choopa kuchotsedwa?

N’chifukwa chiyani nthawi zina ndi bwino kuchepetsa kucheza ndi munthu wochita zoipa ngakhale kuti sanachotsedwe?

Kodi Mkhristu yemwe wanamiziridwa kapena mbiri yake yaipitsidwa angasankhe kuchita chiyani? Nanga n’chifukwa chiyani?

N’chifukwa chiyani Mkhristu wolimba mwauzimu ayenera kulangiza anthu amene akuchita zinthu mopanda nzeru?