Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mantha

Mantha

Kuopa; mantha

De 20:8; Owe 7:3; Miy 29:25

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Eks 32:1-4, 21-24​—Aroni anapanga fano chifukwa chochita mantha anthu atamupanikiza

    • Mko 14:50, 66-72​—Yesu atamangidwa, atumwi onse anamuthawa chifukwa choopa anthu, nayenso Petulo anakana Khristu chifukwa cha mantha

  • Malemba otonthoza:

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakutonthozeni:

    • 2Mb 20:1-17, 22-24​—Mfumu Yehosafati ndi anthu ake anaopa chigulu cha adani awo chomwe chinali champhamvu, koma Yehova analimbikitsa ndi kupulumutsa atumiki ake

    • Lu 12:4-12​—Yesu anaphunzitsa otsatira ake kuti sayenera kuopa anthu kapenanso kudera nkhawa ndi zimene akayankhe akuluakulu a boma chifukwa Yehova adzawathandiza