Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Chipatso cha Mzimu

Chipatso cha Mzimu

Kodi mzimu wa Mulungu umatithandiza kukhala ndi makhalidwe ati? Nanga n’chifukwa chiyani tifunika kukhala odzichepetsa kuti Mulungu atipatse mzimu wake?

Aga 5:22, 23; Yak 4:6

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Sl 143:1, 4-11​—Pa nthawi imene Mfumu Davide anavutika kwambiri, ankaganizira ntchito za Yehova komanso anapemphera kuti amupatse mzimu woyera

    • Lu 11:9-13​—Yesu anagwiritsa ntchito fanizo potikumbutsa kuti Yehova ndi wofunitsitsa kupereka mzimu wake woyera kwa amene amupempha