Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kuwolowa Manja

Kuwolowa Manja

Miy 11:25; Mac 20:35; 2Ak 9:11

Onaninso Miy 19:17; Mt 10:8; Lu 6:38

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 1Mb 22:6-16​—Mfumu Davide anapereka mowolowa manja zinthu zothandizira kumanga kachisi ngakhale kuti sanaloledwe kumanga nawo

    • 1Mf 17:8-16​—Mkazi wamasiye wa ku Zarefati anapatsa mneneri Eliya chakudya ngakhale kuti chinali chomwecho chimene akanadya iyeyo ndi mwana wake