Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Ubwino

Ubwino

Kodi timadziwa bwanji kuti Yehova ndi wabwino?

Sl 25:8; 31:19; 3Yo 11

Onaninso Yer 31:12, 13; Zek 9:16, 17

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Eks 33:17-20; 34:5-7​—Yehova anasonyeza mneneri Mose masomphenya omwe anamuthandiza kuzindikira kuti Yehova ndi wabwino, ndipo anamvanso za makhalidwe a Yehova ambiri odabwitsa

    • Mko 10:17, 18​—Yesu ananena kuti chinthu chilichonse chabwino chimachokera kwa Yehova ndipo Iye ndi amene ali woyenera kutiuza zomwe ndi zabwino

N’chifukwa chiyani tiyenera kukhala ndi khalidwe la ubwino?

Miy 12:2; Aga 6:10; 1At 5:15

Onaninso Aro 15:2, 14; Aef 4:28

  • Nkhani ya m’Baibulo yomwe ingakuthandizeni:

    • Aro 5:7​—Mtumwi Paulo anafotokoza kuti khalidwe la ubwino ndi lofunika kwambiri kuposa kungokhala wolungama