Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Agogo

Agogo
  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 1Mf 15:9-13​—Mfumu Asa anachita zinthu molimba mtima kwambiri pochotsa agogo ake aakazi pa udindo wawo, ndipo sanalole kuti chibale chimulepheretse kukhala wokhulupirika kwa Yehova

    • Miy 13:22​—Agogo okhulupirika amapereka chitsanzo chabwino poika Yehova pamalo oyamba

    • Paulo anayamikira agogo ake a Timoteyo a Loisi, chifukwa cha chikhulupiriro chawo chopanda chinyengo komanso chifukwa chophunzitsa bwino Timoteyo zokhudza Yehova