Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kuona Mtima

Kuona Mtima

De 25:13-16; 2Ak 8:21; Aef 4:25; Ahe 13:18

Onaninso Yob 6:25; Miy 3:32; 6:16-19; 2Ak 6:3, 4, 7, 8

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Sl 15:1-5​—Yehova anafotokoza zinthu zomwe anthu amene angakhale anzake ayenera kuchita ndipo chimodzi mwa zinthuzi ndi kukhala oona mtima

    • Mac 5:1-10​—Hananiya ndi Safira anaphedwa chifukwa chosachita zinthu moona mtima