Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kulambira Mafano

Kulambira Mafano

1Ak 5:11; 10:14; Akl 3:5

Onaninso De 4:25, 26; Yes 42:8; 1Yo 5:21

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Yes 44:9-20​—Yehova anasonyeza kuti kulambira mafano ndi kupanda nzeru

    • Da 3:1-30​—Anyamata a Chiheberi atatu omwe anali anzake a mneneri Danieli analolera kuponyedwa mung’anjo yoyaka moto m’malo molambira mafano