Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Chiwerewere

Chiwerewere

Khalidwe lopanda manyazi; khalidwe limene limadetsa munthu; chigololo

Eks 20:13-17; Mko 7:21-23; 1Ak 6:9, 10, 18; Aga 5:19, 21; Aef 5:5; 1Pe 4:3

Onaninso Le 20:10; Miy 6:32; Aro 13:13; Aef 4:19; 5:3; 2Pe 2:2, 7, 8, 18, 19

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ge 39:7-12​—Mkazi wa Potifara ankamukakamiza Yosefe mobwerezabwereza kuti agone naye, koma iye nthawi zonse ankakana

    • 2Sa 12:7-14​—Mfumu Davide atachita chigololo ndi Bati-seba, banja lake linavutika kwa zaka zambiri