Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kusakondera

Kusakondera

Miy 28:21; Aro 2:11; Yak 3:17

Onaninso Le 19:15; 2Mb 19:6, 7; 1Pe 1:17

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 1Sa 16:4-13​—Pa nthawi imene Samueli ankadzoza mfumu yotsatira ya Isiraeli, Yehova anamulangiza kuti asamaweruze ena potengera maonekedwe