Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Makolo a Mwamuna Kapena Mkazi wanu

Makolo a Mwamuna Kapena Mkazi wanu

N’chifukwa chiyani makolo sayenera kulowelera za m’banja la mwana wawo?

Ge 2:24; Mt 19:4, 5

Onaninso Sl 34:14; Mt 5:9; Aro 12:18; 14:10-13

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Eks 18:1-27​—Mneneri Mose ankalemekezana kwambiri ndi apongozi ake, a Yetero