Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Nsanje

Nsanje

Nsanje

Miy 14:30; 1Ak 13:4

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ge 4:3-8​—Kaini anachitira nsanje Abele kenako anakwiya mumtima mwake mpaka anapha m’bale wakeyo

    • Ge 37:9-11​—Abale ake a Yosefe anamuchitira nsanje

    • 1Sa 18:6-9​—Mfumu Sauli anayamba kukayikira Davide chifukwa choti ankamuchitira nsanje

Nsanje; kaduka

N’chiyani chingatithandize kuti tizipewa kuchita nsanje?