Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Chimwemwe

Chimwemwe

N’chiyani chikusonyeza kuti Yehova ndi Mulungu wachimwemwe?

Kodi ndi zifukwa ziti zimene zimatichititsa kukhala osangalala?

Sl 100:2; Mla 8:15; Yes 65:14, 18; Afi 4:1, 4

Onaninso Sl 64:10; Yes 61:10; Mt 5:11, 12

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Sl 16:7-9, 11​—Wamasalimo Davide anali wosangalala chifukwa chokhala pa ubwenzi wabwino ndi Yehova

    • Ahe 12:1-3​—Mtumwi Paulo anafotokoza kuti nafenso, mofanana ndi Yesu, tikhoza kukhala osangalala ngakhale kuti tili munthawi yovuta chifukwa cha chiyembekezo chomwe tili nacho