Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kukoma Mtima

Kukoma Mtima

Kodi timaona umboni wotani wosonyeza kuti Yehova ndi wokoma mtima?

Aro 3:23, 24; Tit 3:3-6; Ahe 2:9; 1Pe 5:5

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Yon 3:10; 4:11​—Yehova anakomera mtima anthu a ku Nineve omwe analapa ndipo anamveranso chisoni ziweto zawo

    • Lu 6:32-36​—Yesu anatiphunzitsa kuti tizikomerana mtima potikumbutsa kuti Yehova amakomera mtima anthu onse ngakhalenso osayamika ndiponso oipa

Kodi tingasonyeze bwanji kukoma mtima kwa anthu ena?

Miy 19:17; 22:9; Lu 6:35; Aef 4:32

Onaninso Miy 11:17; 31:10, 26; Ahe 13:16

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Mko 14:3-9; Yoh 12:3​—Yesu anayamikira Mariya mlongo wake wa Lazaro chifukwa chochita zinthu mokoma mtima

    • 2Ti 1:16-18​—Onesiforo analimbikitsa mtumwi Paulo pa nthawi yomwe anali m’ndende