Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kukula Mwauzimu

Kukula Mwauzimu

N’chifukwa chiyani Mkhristu aliyense ayenera kuyesetsa kuti akhale wamkulu mwauzimu?

Kodi kudziwa Malemba kungatithandize bwanji kuti tikhale aakulu mwauzimu?

Kodi kukhala wamkulu mwauzimu kumadalira kuchuluka kwa zaka zimene munthu ali nazo?

Yob 32:9; 1Ti 4:12

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Da 1:6-20​—Ngakhale kuti Danieli ndi anzake atatu aja anali aang’ono m’zaka, anali aakulu mwauzimu komanso okhulupirika kwa Yehova

    • Mac 16:1-5​—Timoteyo ali ndi zaka za m’ma 20, abale ankamukhulupirira kuti akwanitsa udindo waukulu umene anapatsidwa mumpingo

Kodi kuchita zinthu limodzi ndi Akhristu anzathu mumpingo kungatithandize bwanji?

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timaona zinthu mwauzimu pa moyo wathu?

N’chifukwa chiyani amuna olimba mwauzimu amavomera kupatsidwa maudindo owonjezereka mumpingo?

Kodi ndi njira yokhayo iti imene ingatithandize kuti tikhale aakulu mwauzimu komanso kuti tiwonjezere luso lolalikira ndi kuphunzitsa?

Lu 21:14, 15; 1Ak 2:6, 10-13

Onaninso Lu 11:13

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Mt 10:19, 20​—Yesu anatsimikizira otsatira ake kuti mzimu woyera udzawathandiza kudziwa zoyenera kulankhula pa nthawi imene akumana ndi mayesero