Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mtendere

Mtendere

Kodi timadziwa bwanji kuti Yehova amaona kuti mtendere ndi wofunika kwambiri?

Kodi tingatani kuti tikhale amtendere komanso kuti tizikhala mwamtendere ndi anthu ena?

Sl 119:165; Yes 48:17, 18; Aro 12:17-21; Afi 4:6-9

Onaninso Yoh 16:33; Aef 6:14, 15; Akl 3:15

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ge 32:9-21; 33:1-4​—Yakobo anachita zambiri kuti akhazikitse mtendere ndi m’bale wake Esau

    • Mt 5:23-26​—Yesu anafotokoza ubwino wokhala mwamtendere komanso chifukwa chake tifunika kumakhala mwamtendere ndi anthu ena